Genesis 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Mulungu anati: “Ndithu Sara mkazi wako adzakuberekera mwana wamwamuna ndipo udzamʼpatse dzina lakuti Isaki.*+ Ndidzakhazikitsa pangano ndi iye, kuti likhale pangano losatha kwa mbadwa zake.+ Aroma 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso sikuti onse ndi ana chifukwa choti ndi mbadwa* za Abulahamu.+ Koma Malemba amati, “Mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.”+ Aheberi 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anali wokonzeka kuchita zimenezo ngakhale kuti anali atauzidwa kuti: “Mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.”+
19 Ndiyeno Mulungu anati: “Ndithu Sara mkazi wako adzakuberekera mwana wamwamuna ndipo udzamʼpatse dzina lakuti Isaki.*+ Ndidzakhazikitsa pangano ndi iye, kuti likhale pangano losatha kwa mbadwa zake.+
7 Ndiponso sikuti onse ndi ana chifukwa choti ndi mbadwa* za Abulahamu.+ Koma Malemba amati, “Mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.”+
18 Anali wokonzeka kuchita zimenezo ngakhale kuti anali atauzidwa kuti: “Mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.”+