Genesis 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma pa tsiku lachitatu, anthuwo akumvabe ululu, ana awiri a Yakobo, Simiyoni ndi Levi, alongo ake a Dina,+ aliyense anatenga lupanga lake nʼkukalowa mumzindawo anthuwo asakuyembekezera ndipo anapha mwamuna aliyense.+ Genesis 49:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Simiyoni ndi Levi mʼpachibale.+ Malupanga awo ndi zida zochitira zachiwawa.+ 1 Mbiri 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ana a Simiyoni+ anali Nemueli, Yamini, Yaribi, Zera ndi Shauli.+
25 Koma pa tsiku lachitatu, anthuwo akumvabe ululu, ana awiri a Yakobo, Simiyoni ndi Levi, alongo ake a Dina,+ aliyense anatenga lupanga lake nʼkukalowa mumzindawo anthuwo asakuyembekezera ndipo anapha mwamuna aliyense.+