Genesis 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamwamba pa masitepewo anaonapo Yehova, amene anamuuza kuti: “Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abulahamu kholo lako ndi Mulungu wa Isaki.+ Dziko limene wagonapoli ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbadwa* zako.+ Genesis 31:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndikanatha kukuchitirani zoipa, koma Mulungu wa bambo anu analankhula nane usiku wapitawu kuti, ‘Usamale ndi zimene ukalankhule ndi Yakobo, kaya zabwino kapena zoipa.’+
13 Pamwamba pa masitepewo anaonapo Yehova, amene anamuuza kuti: “Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abulahamu kholo lako ndi Mulungu wa Isaki.+ Dziko limene wagonapoli ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbadwa* zako.+
29 Ndikanatha kukuchitirani zoipa, koma Mulungu wa bambo anu analankhula nane usiku wapitawu kuti, ‘Usamale ndi zimene ukalankhule ndi Yakobo, kaya zabwino kapena zoipa.’+