28 Kenako munthu wa Mulungu woona uja anapita kwa mfumu ya Isiraeli nʼkunena kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Popeza Asiriya anena kuti: “Yehova ndi Mulungu wa mapiri, osati Mulungu wa zigwa,” ndipereka chigulu chonsechi mʼmanja mwako+ ndipo anthu inu mudziwadi kuti ine ndine Yehova.’”+