Deuteronomo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova Mulungu wanu musamamuyese+ ngati mmene munamuyesera ku Masa.+ Salimo 95:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Musaumitse mitima yanu ngati mmene makolo anu anachitira ku Meriba,*+Ngati mmene anachitira ku Masa* mʼchipululu,+ 9 Pamene makolo anu anandiyesa.+Iwo anatsutsana ndi ine ngakhale kuti anaona ntchito zanga.+ Aheberi 3:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 musaumitse mitima yanu ngati mmene zinakhalira pamene makolo anu anandipsetsa mtima kwambiri, ngati mmene zinalili pa tsiku limene anandiyesa mʼchipululu.+ 9 Mʼchipululumo, makolo anu anandiyesa ngakhale kuti anali ataona ntchito zanga kwa zaka 40.+
8 Musaumitse mitima yanu ngati mmene makolo anu anachitira ku Meriba,*+Ngati mmene anachitira ku Masa* mʼchipululu,+ 9 Pamene makolo anu anandiyesa.+Iwo anatsutsana ndi ine ngakhale kuti anaona ntchito zanga.+
8 musaumitse mitima yanu ngati mmene zinakhalira pamene makolo anu anandipsetsa mtima kwambiri, ngati mmene zinalili pa tsiku limene anandiyesa mʼchipululu.+ 9 Mʼchipululumo, makolo anu anandiyesa ngakhale kuti anali ataona ntchito zanga kwa zaka 40.+