Ekisodo 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno anthu anayamba kukangana ndi Mose+ kuti: “Tipatse madzi timwe.” Koma Mose anawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukukangana ndi ine? Nʼchifukwa chiyani mukupitiriza kuyesa Yehova?”+ Ekisodo 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho iye anatchula malowo kuti Masa*+ ndi Meriba,*+ chifukwa Aisiraeli anakangana ndi Mose komanso chifukwa chakuti anayesa Yehova+ kuti: “Kodi pakati pathu pano, Yehova alipo kapena ayi?” Salimo 95:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Musaumitse mitima yanu ngati mmene makolo anu anachitira ku Meriba,*+Ngati mmene anachitira ku Masa* mʼchipululu,+ 9 Pamene makolo anu anandiyesa.+Iwo anatsutsana ndi ine ngakhale kuti anaona ntchito zanga.+ Aheberi 3:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 musaumitse mitima yanu ngati mmene zinakhalira pamene makolo anu anandipsetsa mtima kwambiri, ngati mmene zinalili pa tsiku limene anandiyesa mʼchipululu.+ 9 Mʼchipululumo, makolo anu anandiyesa ngakhale kuti anali ataona ntchito zanga kwa zaka 40.+
2 Ndiyeno anthu anayamba kukangana ndi Mose+ kuti: “Tipatse madzi timwe.” Koma Mose anawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukukangana ndi ine? Nʼchifukwa chiyani mukupitiriza kuyesa Yehova?”+
7 Choncho iye anatchula malowo kuti Masa*+ ndi Meriba,*+ chifukwa Aisiraeli anakangana ndi Mose komanso chifukwa chakuti anayesa Yehova+ kuti: “Kodi pakati pathu pano, Yehova alipo kapena ayi?”
8 Musaumitse mitima yanu ngati mmene makolo anu anachitira ku Meriba,*+Ngati mmene anachitira ku Masa* mʼchipululu,+ 9 Pamene makolo anu anandiyesa.+Iwo anatsutsana ndi ine ngakhale kuti anaona ntchito zanga.+
8 musaumitse mitima yanu ngati mmene zinakhalira pamene makolo anu anandipsetsa mtima kwambiri, ngati mmene zinalili pa tsiku limene anandiyesa mʼchipululu.+ 9 Mʼchipululumo, makolo anu anandiyesa ngakhale kuti anali ataona ntchito zanga kwa zaka 40.+