Deuteronomo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Musankhe oweruza+ ndi atsogoleri a fuko lililonse mʼmizinda yonse imene* Yehova Mulungu wanu akukupatsani ndipo aziweruza anthu mwachilungamo. Deuteronomo 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 anthu awiri amene akukanganawo aziima pamaso pa Yehova, kapena kuti pamaso pa ansembe ndi oweruza amene akuweruza masiku amenewo.+
18 Musankhe oweruza+ ndi atsogoleri a fuko lililonse mʼmizinda yonse imene* Yehova Mulungu wanu akukupatsani ndipo aziweruza anthu mwachilungamo.
17 anthu awiri amene akukanganawo aziima pamaso pa Yehova, kapena kuti pamaso pa ansembe ndi oweruza amene akuweruza masiku amenewo.+