Deuteronomo 27:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ‘Wotembereredwa ndi munthu wopotoza chiweruzo cha mlendo+ amene akukhala pakati panu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’) Yakobo 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kulambira* koyera komanso kosadetsedwa kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ amene akukumana ndi mavuto*+ komanso kupewa kuti dzikoli likuchititseni kukhala ndi banga.+
19 ‘Wotembereredwa ndi munthu wopotoza chiweruzo cha mlendo+ amene akukhala pakati panu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
27 Kulambira* koyera komanso kosadetsedwa kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ amene akukumana ndi mavuto*+ komanso kupewa kuti dzikoli likuchititseni kukhala ndi banga.+