Yoswa 21:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Yehova anachititsa kuti azikhala mwamtendere mʼdzikolo, mogwirizana ndi zonse zimene analumbirira makolo awo.+ Panalibe mdani aliyense amene anatha kulimbana nawo.+ Yehova anapereka adani awo onse mʼmanja mwawo.+ Yoswa 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano Yoswa anali atakalamba ndiponso anali ndi zaka zambiri.+ Apa nʼkuti patapita masiku ambiri kuchokera pamene Yehova anapatsa Aisiraeli mpumulo+ powapulumutsa kwa adani awo onse owazungulira.
44 Yehova anachititsa kuti azikhala mwamtendere mʼdzikolo, mogwirizana ndi zonse zimene analumbirira makolo awo.+ Panalibe mdani aliyense amene anatha kulimbana nawo.+ Yehova anapereka adani awo onse mʼmanja mwawo.+
23 Tsopano Yoswa anali atakalamba ndiponso anali ndi zaka zambiri.+ Apa nʼkuti patapita masiku ambiri kuchokera pamene Yehova anapatsa Aisiraeli mpumulo+ powapulumutsa kwa adani awo onse owazungulira.