Ekisodo 33:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Mulungu anati: “Ineyo ndipita nawe+ ndipo ndidzakupatsa mpumulo.”+ Levitiko 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzakupatsani mtendere mʼdzikolo,+ moti mudzagona pansi popanda wokuopsezani.+ Ndidzachotsa zilombo zoopsa zakutchire mʼdziko lanu, ndipo palibe amene adzachite nanu nkhondo. Yoswa 21:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Yehova anachititsa kuti azikhala mwamtendere mʼdzikolo, mogwirizana ndi zonse zimene analumbirira makolo awo.+ Panalibe mdani aliyense amene anatha kulimbana nawo.+ Yehova anapereka adani awo onse mʼmanja mwawo.+
6 Ndidzakupatsani mtendere mʼdzikolo,+ moti mudzagona pansi popanda wokuopsezani.+ Ndidzachotsa zilombo zoopsa zakutchire mʼdziko lanu, ndipo palibe amene adzachite nanu nkhondo.
44 Yehova anachititsa kuti azikhala mwamtendere mʼdzikolo, mogwirizana ndi zonse zimene analumbirira makolo awo.+ Panalibe mdani aliyense amene anatha kulimbana nawo.+ Yehova anapereka adani awo onse mʼmanja mwawo.+