Ekisodo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Mose anafunsa Mulungu woona kuti: “Nditati ndapita kwa Aisiraeli nʼkuwauza kuti, ‘Mulungu wa makolo anu wandituma kwa inu,’ iwo nʼkundifunsa kuti, ‘Dzina lake ndi ndani?’+ Ndikawayankhe kuti chiyani?” Ekisodo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinkaonekera kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse kwa iwo.+ Ekisodo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wokoma mtima,*+ wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka+ komanso choonadi.*+
13 Koma Mose anafunsa Mulungu woona kuti: “Nditati ndapita kwa Aisiraeli nʼkuwauza kuti, ‘Mulungu wa makolo anu wandituma kwa inu,’ iwo nʼkundifunsa kuti, ‘Dzina lake ndi ndani?’+ Ndikawayankhe kuti chiyani?”
3 Ndinkaonekera kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse kwa iwo.+
6 Ndiyeno Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wokoma mtima,*+ wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka+ komanso choonadi.*+