Ekisodo 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova ndi msilikali wamphamvu.+ Dzina lake ndi Yehova.+ Salimo 96:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mʼpatseni Yehova ulemerero woyenera dzina lake.+Bweretsani mphatso ndi kulowa mʼmabwalo ake. Salimo 135:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu Yehova, dzina lanu lidzakhalapo kwamuyaya. Inu Yehova, dzina lanu lidzakhalapo* ku mibadwo yonse.+ Hoseya 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba,+Amakumbukiridwa ndi dzina lakuti Yehova.+ Yohane 17:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ine ndachititsa kuti iwo adziwe dzina lanu ndipo ndidzapitiriza kuwadziwitsa dzinalo+ kuti iwonso azisonyeza chikondi ngati chimene inu munandisonyeza, kuti inenso ndikhale wogwirizana ndi iwo.”+ Aroma 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa “aliyense woitana pa dzina la Yehova* adzapulumuka.”+
13 Inu Yehova, dzina lanu lidzakhalapo kwamuyaya. Inu Yehova, dzina lanu lidzakhalapo* ku mibadwo yonse.+
26 Ine ndachititsa kuti iwo adziwe dzina lanu ndipo ndidzapitiriza kuwadziwitsa dzinalo+ kuti iwonso azisonyeza chikondi ngati chimene inu munandisonyeza, kuti inenso ndikhale wogwirizana ndi iwo.”+