8 Apatuka mofulumira panjira imene ndinawalamula kuti aziyendamo.+ Iwo adzipangira fano la mwana wa ngʼombe. Akuligwadira komanso kupereka nsembe kwa fanolo ndipo akunena kuti, ‘Aisiraeli inu, uyu ndi Mulungu wanu amene anakutsogolerani potuluka mʼdziko la Iguputo.’”