Levitiko 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Musapange milungu yopanda pake,+ chifaniziro,+ kapena chipilala chopatulika kuti muzichilambira. Musaike mwala wogoba+ mʼdziko lanu kuti muziugwadira,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu. Salimo 96:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake,+Koma Yehova ndi amene anapanga kumwamba.+ Habakuku 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi chifaniziro chosema chili ndi phindu lanji,Pamene munthu wachisema? Nanga chifaniziro chachitsulo ndi mphunzitsi wonama zili ndi phindu lanji,Ngakhale kuti wochipanga amachikhulupirira,Nʼkumapanga milungu yopanda pake yosalankhula?+ 1 Akorinto 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho okondedwa anga, pewani* kulambira mafano.+
26 “‘Musapange milungu yopanda pake,+ chifaniziro,+ kapena chipilala chopatulika kuti muzichilambira. Musaike mwala wogoba+ mʼdziko lanu kuti muziugwadira,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.
5 Milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake,+Koma Yehova ndi amene anapanga kumwamba.+
18 Kodi chifaniziro chosema chili ndi phindu lanji,Pamene munthu wachisema? Nanga chifaniziro chachitsulo ndi mphunzitsi wonama zili ndi phindu lanji,Ngakhale kuti wochipanga amachikhulupirira,Nʼkumapanga milungu yopanda pake yosalankhula?+