Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wopha munthu, nayenso adzaphedwa ndi munthu,*+ chifukwa Mulungu anapanga munthu mʼchifaniziro chake.+ Ekisodo 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Aliyense amene wamenya munthu mpaka munthuyo kufa ayenera kuphedwa.+
6 Aliyense wopha munthu, nayenso adzaphedwa ndi munthu,*+ chifukwa Mulungu anapanga munthu mʼchifaniziro chake.+