11 Iye analonjeza kuti: “Inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, mukaona kuvutika kwa ine kapolo wanu nʼkundikumbukira ndiponso mukapanda kundiiwala ine kapolo wanu nʼkundipatsa mwana wamwamuna,+ ndidzamʼpereka kwa Yehova masiku onse a moyo wake ndipo lezala silidzadutsa mʼmutu mwake.”+