1 Samueli 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mwanayo atangosiya kuyamwa, Hana anapita naye ku Silo atatenga ngʼombe yaingʼono yamphongo yazaka zitatu, ufa wokwana muyezo umodzi wa efa* ndi mtsuko wa vinyo.+ Iye analowa mʼnyumba ya Yehova ku Silo+ limodzi ndi mwanayo.
24 Mwanayo atangosiya kuyamwa, Hana anapita naye ku Silo atatenga ngʼombe yaingʼono yamphongo yazaka zitatu, ufa wokwana muyezo umodzi wa efa* ndi mtsuko wa vinyo.+ Iye analowa mʼnyumba ya Yehova ku Silo+ limodzi ndi mwanayo.