Levitiko 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati akupereka nsembe chifukwa cha lonjezo limene anapanga+ kapena ngati akupereka nsembe yaufulu,+ aziidya pa tsiku limene wapereka nsembeyo, ndipo yotsala angathenso kuidya pa tsiku lotsatira. Levitiko 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ngati munthu akupereka nsembe yamgwirizano+ kwa Yehova kuti akwaniritse lonjezo lake kapena kuti ikhale nsembe yaufulu, azipereka ngʼombe kapena nkhosa yopanda chilema, kuti Mulungu ailandire. Izikhala yopanda chilema chilichonse.
16 Ngati akupereka nsembe chifukwa cha lonjezo limene anapanga+ kapena ngati akupereka nsembe yaufulu,+ aziidya pa tsiku limene wapereka nsembeyo, ndipo yotsala angathenso kuidya pa tsiku lotsatira.
21 Ngati munthu akupereka nsembe yamgwirizano+ kwa Yehova kuti akwaniritse lonjezo lake kapena kuti ikhale nsembe yaufulu, azipereka ngʼombe kapena nkhosa yopanda chilema, kuti Mulungu ailandire. Izikhala yopanda chilema chilichonse.