Numeri 26:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ana aamuna a Manase+ anali Makiri+ amene anali kholo la banja la Amakiri. Makiri anabereka Giliyadi. Giliyadi anali kholo la banja la Agiliyadi.+
29 Ana aamuna a Manase+ anali Makiri+ amene anali kholo la banja la Amakiri. Makiri anabereka Giliyadi. Giliyadi anali kholo la banja la Agiliyadi.+