1 Akorinto 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zinthu zimenezi ndi zitsanzo kwa ife, kuti nafenso tisamalakelake zinthu zoipa ngati mmene iwo anachitira.+ 1 Akorinto 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tisakhalenso ongʼungʼudza, ngati mmene ena a iwo anachitira,+ nʼkuphedwa ndi mngelo wowononga.+ Yuda 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zonsezi, ndikufuna kukukumbutsani kuti Yehova* atapulumutsa anthu ake powatulutsa mʼdziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+
6 Zinthu zimenezi ndi zitsanzo kwa ife, kuti nafenso tisamalakelake zinthu zoipa ngati mmene iwo anachitira.+
5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zonsezi, ndikufuna kukukumbutsani kuti Yehova* atapulumutsa anthu ake powatulutsa mʼdziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+