Ekisodo 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno mʼtsogolo ana anu akadzakufunsani kuti, ‘Kodi zimenezi zikutanthauza chiyani?’ mudzawayankhe kuti, ‘Yehova anatitulutsa ndi dzanja lake lamphamvu mu Iguputo, mʼnyumba ya ukapolo.+ Salimo 44:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Inu Mulungu, ife tamva ndi makutu athu,Makolo athu anatifotokozera+Ntchito zimene inu munachita mu nthawi yawo,Mʼmasiku akale.
14 Ndiyeno mʼtsogolo ana anu akadzakufunsani kuti, ‘Kodi zimenezi zikutanthauza chiyani?’ mudzawayankhe kuti, ‘Yehova anatitulutsa ndi dzanja lake lamphamvu mu Iguputo, mʼnyumba ya ukapolo.+
44 Inu Mulungu, ife tamva ndi makutu athu,Makolo athu anatifotokozera+Ntchito zimene inu munachita mu nthawi yawo,Mʼmasiku akale.