Deuteronomo 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma dziko limene mwatsala pangʼono kuwolokerako nʼkukalitenga kuti likhale lanu ndi dziko lamapiri ndi zigwa.+ Limamwa madzi a mvula amene amagwa kuchokera kumwamba.+
11 Koma dziko limene mwatsala pangʼono kuwolokerako nʼkukalitenga kuti likhale lanu ndi dziko lamapiri ndi zigwa.+ Limamwa madzi a mvula amene amagwa kuchokera kumwamba.+