Deuteronomo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tembenukani mulowere kudera lamapiri la Aamori+ komanso kwa anthu onse oyandikana nawo okhala ku Araba,+ kudera lamapiri, ku Sefela, ku Negebu, mʼmbali mwa nyanja,+ mʼdziko la Akanani ndi ku Lebanoni*+ mpaka kumtsinje waukulu wa Firate.+
7 Tembenukani mulowere kudera lamapiri la Aamori+ komanso kwa anthu onse oyandikana nawo okhala ku Araba,+ kudera lamapiri, ku Sefela, ku Negebu, mʼmbali mwa nyanja,+ mʼdziko la Akanani ndi ku Lebanoni*+ mpaka kumtsinje waukulu wa Firate.+