Ekisodo 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Musadzaweramire milungu yawo kapena kuitumikira, ndipo musadzatengere zochita zawo.+ Mʼmalomwake, mudzawononge mafano awo komanso kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Ekisodo 34:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma maguwa awo ansembe mukawagwetse, zipilala zawo zopatulika mukaziphwanye ndipo mizati* yawo yopatulika mukaidule.+
24 Musadzaweramire milungu yawo kapena kuitumikira, ndipo musadzatengere zochita zawo.+ Mʼmalomwake, mudzawononge mafano awo komanso kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+
13 Koma maguwa awo ansembe mukawagwetse, zipilala zawo zopatulika mukaziphwanye ndipo mizati* yawo yopatulika mukaidule.+