Ekisodo 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Sindidzawathamangitsa pamaso panu mʼchaka chimodzi, kuti dzikolo lisakhale bwinja ndiponso kuti zilombo zakutchire zisachuluke nʼkukuvutitsani.+ Deuteronomo 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Lero ndichititsa kuti anthu onse okhala pansi pa thambo, amene amva za inu, achite nanu mantha kwambiri nʼkuyamba kukuopani. Iwo adzasokonezeka maganizo ndipo adzanjenjemera* chifukwa cha inu.’+ Yoswa 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo anawauza kuti: “Ndikudziwa kuti Yehova akupatsani dzikoli+ ndipo tonse tikuchita nanu mantha.+ Aliyense mʼdzikoli mtima wake suli mʼmalo chifukwa cha inu.+ Yoswa 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndinawachititsa mantha inu musanafike, choncho anakuthawani+ ngati mmene anachitira mafumu awiri a Aamori. Iwo sanathawe chifukwa cha lupanga lanu kapena chifukwa cha uta wanu.+
29 Sindidzawathamangitsa pamaso panu mʼchaka chimodzi, kuti dzikolo lisakhale bwinja ndiponso kuti zilombo zakutchire zisachuluke nʼkukuvutitsani.+
25 Lero ndichititsa kuti anthu onse okhala pansi pa thambo, amene amva za inu, achite nanu mantha kwambiri nʼkuyamba kukuopani. Iwo adzasokonezeka maganizo ndipo adzanjenjemera* chifukwa cha inu.’+
9 Ndipo anawauza kuti: “Ndikudziwa kuti Yehova akupatsani dzikoli+ ndipo tonse tikuchita nanu mantha.+ Aliyense mʼdzikoli mtima wake suli mʼmalo chifukwa cha inu.+
12 Ndinawachititsa mantha inu musanafike, choncho anakuthawani+ ngati mmene anachitira mafumu awiri a Aamori. Iwo sanathawe chifukwa cha lupanga lanu kapena chifukwa cha uta wanu.+