5 Koma mukaonetsetse kuti mukutsatira Chilamulo ndiponso malamulo amene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulani.+ Muzikakonda Yehova Mulungu wanu,+ kuyenda mʼnjira zake zonse,+ kumvera malamulo ake,+ kumʼmamatira+ ndiponso kumʼtumikira+ ndi mtima wanu wonse komanso moyo wanu wonse.”+