-
Deuteronomo 12:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Muzidzabweretsa zinthu zonse zimene ndikukulamulani kumalo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe kuti kukhale dzina lake.+ Muzidzabweretsa nsembe zanu zopsereza ndi nsembe zina, zopereka zanu za chakhumi,+ chopereka chochokera mʼmanja mwanu ndi nsembe zonse zimene mukupereka pokwaniritsa lonjezo limene munachita kwa Yehova.
-