Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+ Agalatiya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Onse amene amadalira ntchito za chilamulo ndi otembereredwa, chifukwa Malemba amati: “Munthu aliyense amene sakupitiriza kutsatira zinthu zonse zimene zinalembedwa mumpukutu wa Chilamulo ndi wotembereredwa.”+
15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+
10 Onse amene amadalira ntchito za chilamulo ndi otembereredwa, chifukwa Malemba amati: “Munthu aliyense amene sakupitiriza kutsatira zinthu zonse zimene zinalembedwa mumpukutu wa Chilamulo ndi wotembereredwa.”+