Levitiko 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzakudalitsani,* kukuchititsani kuti mubereke ana ambiri komanso kukuchulukitsani.+ Ndipo ndidzasunga pangano langa ndi inu.+ Salimo 127:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndi mphoto yochokera kwa Mulungu.+ Salimo 128:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mkazi wako adzakhala ngati mtengo wa mpesa wobereka zipatso mʼnyumba mwako.+Ana ako adzakhala ngati mphukira za mtengo wa maolivi kuzungulira tebulo lako.
9 Ndidzakudalitsani,* kukuchititsani kuti mubereke ana ambiri komanso kukuchulukitsani.+ Ndipo ndidzasunga pangano langa ndi inu.+
3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndi mphoto yochokera kwa Mulungu.+
3 Mkazi wako adzakhala ngati mtengo wa mpesa wobereka zipatso mʼnyumba mwako.+Ana ako adzakhala ngati mphukira za mtengo wa maolivi kuzungulira tebulo lako.