Salimo 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo sanatenge dzikolo pogwiritsa ntchito lupanga lawo.+Ndipo si mkono wawo umene unachititsa kuti apambane.+ Koma zimenezi zinatheka chifukwa cha dzanja lanu lamanja,+ mkono wanu ndi kuwala kwa nkhope yanu,Chifukwa munkasangalala nawo.+
3 Iwo sanatenge dzikolo pogwiritsa ntchito lupanga lawo.+Ndipo si mkono wawo umene unachititsa kuti apambane.+ Koma zimenezi zinatheka chifukwa cha dzanja lanu lamanja,+ mkono wanu ndi kuwala kwa nkhope yanu,Chifukwa munkasangalala nawo.+