Yoswa 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amunawo anayankha kuti: “Tikadzapanda kusunga lonjezo lathu, ifeyo tidzafe mʼmalo mwa inu. Mukapanda kuulula nkhaniyi, Yehova akadzatipatsa dzikoli, ifenso tidzakusonyezani kukoma mtima* ndipo tidzakhala okhulupirika.” Aheberi 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa cha chikhulupiriro, Rahabi amene anali hule uja sanaphedwe limodzi ndi anthu osamvera, chifukwa iye analandira mwamtendere anthu amene anakafufuza za mzindawo.+
14 Amunawo anayankha kuti: “Tikadzapanda kusunga lonjezo lathu, ifeyo tidzafe mʼmalo mwa inu. Mukapanda kuulula nkhaniyi, Yehova akadzatipatsa dzikoli, ifenso tidzakusonyezani kukoma mtima* ndipo tidzakhala okhulupirika.”
31 Chifukwa cha chikhulupiriro, Rahabi amene anali hule uja sanaphedwe limodzi ndi anthu osamvera, chifukwa iye analandira mwamtendere anthu amene anakafufuza za mzindawo.+