Numeri 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Tenga Yoswa mwana wa Nuni, munthu wolimba mtima,* ndipo uike dzanja lako pa iye.+ Numeri 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Umupatseko mphamvu zako,*+ kuti gulu lonse la Aisiraeli lizimumvera.+ Deuteronomo 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yoswa mwana wa Nuni anali atadzazidwa ndi mzimu wa nzeru, chifukwa Mose anaika manja ake pa iye.+ Aisiraeli anayamba kumumvera ndipo anachita mogwirizana ndi zomwe Yehova analamula Mose.+
18 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Tenga Yoswa mwana wa Nuni, munthu wolimba mtima,* ndipo uike dzanja lako pa iye.+
9 Yoswa mwana wa Nuni anali atadzazidwa ndi mzimu wa nzeru, chifukwa Mose anaika manja ake pa iye.+ Aisiraeli anayamba kumumvera ndipo anachita mogwirizana ndi zomwe Yehova analamula Mose.+