Numeri 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Powatumiza kuti akazonde dziko la Kanani, Mose anawauza kuti: “Mupite kumeneko kudzera ku Negebu, ndipo kenako mukafike kudera lamapiri.+ Deuteronomo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tembenukani mulowere kudera lamapiri la Aamori+ komanso kwa anthu onse oyandikana nawo okhala ku Araba,+ kudera lamapiri, ku Sefela, ku Negebu, mʼmbali mwa nyanja,+ mʼdziko la Akanani ndi ku Lebanoni*+ mpaka kumtsinje waukulu wa Firate.+
17 Powatumiza kuti akazonde dziko la Kanani, Mose anawauza kuti: “Mupite kumeneko kudzera ku Negebu, ndipo kenako mukafike kudera lamapiri.+
7 Tembenukani mulowere kudera lamapiri la Aamori+ komanso kwa anthu onse oyandikana nawo okhala ku Araba,+ kudera lamapiri, ku Sefela, ku Negebu, mʼmbali mwa nyanja,+ mʼdziko la Akanani ndi ku Lebanoni*+ mpaka kumtsinje waukulu wa Firate.+