1 Samueli 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anatumiza Likasa la Mulungu woona ku Ekironi.+ Ndiyeno Likasa la Mulungu woona litangofika ku Ekironi, anthu akumeneko anayamba kulira, kuti: “Atibweretsera Likasa la Mulungu wa Isiraeli kuti atiphe tonse!”+
10 Choncho anatumiza Likasa la Mulungu woona ku Ekironi.+ Ndiyeno Likasa la Mulungu woona litangofika ku Ekironi, anthu akumeneko anayamba kulira, kuti: “Atibweretsera Likasa la Mulungu wa Isiraeli kuti atiphe tonse!”+