-
Numeri 33:54Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
54 Mukagwiritse ntchito maere+ pogawa dzikolo kwa mabanja anu kuti likhale cholowa chanu. Banja la anthu ambiri mukaliwonjezere cholowa chawo, ndipo banja la anthu ochepa mukalichepetsere cholowa chawo.+ Banja lililonse mukalipatse cholowa mogwirizana ndi kumene maere a banjalo agwera. Mukalandira malo kuti akhale cholowa chanu potsata mafuko a makolo anu.+
-