Deuteronomo 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova adzachititsa adani anu amene adzakuukireni kugonja pamaso panu.+ Pobwera kudzakuukirani adzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso panu, adzadutsa njira zosiyanasiyana 7.+
7 Yehova adzachititsa adani anu amene adzakuukireni kugonja pamaso panu.+ Pobwera kudzakuukirani adzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso panu, adzadutsa njira zosiyanasiyana 7.+