Yoswa 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yoswa analanda dziko lonselo, dera lamapiri, dera lonse la Negebu,+ dziko lonse la Goseni, ku Sefela,+ ku Araba+ ndiponso dera lamapiri la Isiraeli ndi zigwa zake. Yoswa 21:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Yehova anachititsa kuti azikhala mwamtendere mʼdzikolo, mogwirizana ndi zonse zimene analumbirira makolo awo.+ Panalibe mdani aliyense amene anatha kulimbana nawo.+ Yehova anapereka adani awo onse mʼmanja mwawo.+ Aheberi 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chifukwa cha chikhulupiriro, mpanda wa Yeriko unagwa, anthu atayenda mouzungulira kwa masiku 7.+
16 Yoswa analanda dziko lonselo, dera lamapiri, dera lonse la Negebu,+ dziko lonse la Goseni, ku Sefela,+ ku Araba+ ndiponso dera lamapiri la Isiraeli ndi zigwa zake.
44 Yehova anachititsa kuti azikhala mwamtendere mʼdzikolo, mogwirizana ndi zonse zimene analumbirira makolo awo.+ Panalibe mdani aliyense amene anatha kulimbana nawo.+ Yehova anapereka adani awo onse mʼmanja mwawo.+