Oweruza 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ine ndidzabweretsa kwa iwe kumtsinje* wa Kisoni,+ Sisera mkulu wa gulu lankhondo la Yabini, pamodzi ndi magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake ndipo ndidzamʼpereka mʼmanja mwako.’”+ Oweruza 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nthawi yomweyo, Sisera anasonkhanitsa magaleta ake onse ankhondo, magaleta 900 okhala ndi zitsulo zazitali komanso zakuthwa. Anasonkhanitsanso asilikali ake onse kuchokera ku Haroseti-ha-goimu ndipo anapita kumtsinje* wa Kisoni.+ Salimo 83:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muwachitire zimene munachitira Midiyani,+Komanso zimene munachitira Sisera ndi Yabini kumtsinje wa Kisoni.*+
7 Ine ndidzabweretsa kwa iwe kumtsinje* wa Kisoni,+ Sisera mkulu wa gulu lankhondo la Yabini, pamodzi ndi magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake ndipo ndidzamʼpereka mʼmanja mwako.’”+
13 Nthawi yomweyo, Sisera anasonkhanitsa magaleta ake onse ankhondo, magaleta 900 okhala ndi zitsulo zazitali komanso zakuthwa. Anasonkhanitsanso asilikali ake onse kuchokera ku Haroseti-ha-goimu ndipo anapita kumtsinje* wa Kisoni.+
9 Muwachitire zimene munachitira Midiyani,+Komanso zimene munachitira Sisera ndi Yabini kumtsinje wa Kisoni.*+