-
Oweruza 11:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Koma mkazi wa Giliyadi anamuberekeranso ana aamuna. Anawo atakula, anathamangitsa Yefita nʼkumuuza kuti: “Iwe sudzalandira cholowa mʼnyumba ya bambo athu, chifukwa ndiwe mwana wa mayi wina.”
-