30 Ndiyeno Yefita analonjeza+ Yehova kuti: “Mukapereka Aamoni mʼmanja mwanga, 31 aliyense amene adzatuluka mʼnyumba yanga kudzandichingamira pamene ndikubwera mwamtendere kuchokera kwa Aamoni, ndidzamʼpereka kwa inu Yehova+ kuti akhale nsembe yopsereza.”+