1 Samueli 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zitatero, anthu onse anauza Samueli kuti: “Tipempherereni ife atumiki anu kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa sitikufuna kufa. Tawonjezera choipa china pa machimo athu popempha kuti tikhale ndi mfumu.” Yesaya 37:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwina Yehova Mulungu wanu amva mawu a Rabisake, amene mbuye wake mfumu ya Asuri yamutuma kuti adzanyoze Mulungu wamoyo.+ Ndipo amulanga chifukwa cha mawu amene Yehova Mulungu wanu wamva. Choncho inuyo mupemphere+ mʼmalo mwa anthu amene atsala.’”+
19 Zitatero, anthu onse anauza Samueli kuti: “Tipempherereni ife atumiki anu kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa sitikufuna kufa. Tawonjezera choipa china pa machimo athu popempha kuti tikhale ndi mfumu.”
4 Mwina Yehova Mulungu wanu amva mawu a Rabisake, amene mbuye wake mfumu ya Asuri yamutuma kuti adzanyoze Mulungu wamoyo.+ Ndipo amulanga chifukwa cha mawu amene Yehova Mulungu wanu wamva. Choncho inuyo mupemphere+ mʼmalo mwa anthu amene atsala.’”+