-
1 Mafumu 12:3, 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 ndipo anthu anatumiza uthenga womuitana. Kenako Yerobowamu ndi gulu lonse la Aisiraeli anabwera kwa Rehobowamu nʼkumuuza kuti: 4 “Bambo anu anachititsa kuti goli lathu likhale lowawa.+ Koma inuyo mukatifewetsera ntchito yowawa ya bambo anu komanso goli lolemera limene ankatisenzetsa, tizikutumikirani.”
-