1 Samueli 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Samueli anauza anthu onsewo kuti: “Kodi mwaona munthu amene Yehova wamusankha,+ kuti palibe aliyense wofanana naye?” Anthu onsewo anayamba kufuula kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!” 1 Samueli 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Samueli anati: “Kodi sunkadziona ngati wachabechabe+ utasankhidwa kukhala mtsogoleri wa mafuko a Isiraeli komanso pamene Yehova anakudzoza kuti ukhale mfumu ya Isiraeli?+ Machitidwe 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma kenako anthuwo ananena kuti akufuna mfumu.+ Choncho Mulungu anawapatsa Sauli mwana wa Kisi, munthu wa fuko la Benjamini,+ ndipo anakhala mfumu yawo kwa zaka 40.
24 Ndiyeno Samueli anauza anthu onsewo kuti: “Kodi mwaona munthu amene Yehova wamusankha,+ kuti palibe aliyense wofanana naye?” Anthu onsewo anayamba kufuula kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”
17 Ndiyeno Samueli anati: “Kodi sunkadziona ngati wachabechabe+ utasankhidwa kukhala mtsogoleri wa mafuko a Isiraeli komanso pamene Yehova anakudzoza kuti ukhale mfumu ya Isiraeli?+
21 Koma kenako anthuwo ananena kuti akufuna mfumu.+ Choncho Mulungu anawapatsa Sauli mwana wa Kisi, munthu wa fuko la Benjamini,+ ndipo anakhala mfumu yawo kwa zaka 40.