-
Genesis 19:12, 13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiyeno alendowo anafunsa Loti kuti: “Kodi uli ndi achibale alionse kuno? Uwatulutse mumzinda uno, kaya ndi akamwini ako, ana ako aamuna, ana ako aakazi kapena aliyense amene ndi mʼbale wako. 13 Malo ano tiwawononga chifukwa Yehova wamva madandaulo ambiri okhudza anthuwa,+ moti Yehova watituma kudzawononga mzindawu.”
-