1 Samueli 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Samueli anauza Sauli kuti: “Zimene wachitazi ndi zopusa. Sunamvere lamulo limene Yehova Mulungu wako anakupatsa.+ Ukanamvera, Yehova akanachititsa kuti banja lako lilamulire Isiraeli mpaka kalekale. 1 Samueli 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano pita ukaphe Aamaleki+ ndiponso kuwononga+ zinthu zonse zimene ali nazo. Usakasiye aliyense.* Ukaphe+ mwamuna ndi mkazi, mwana wamngʼono ndi wakhanda, ngʼombe ndi nkhosa komanso ngamila ndi bulu.’”+
13 Koma Samueli anauza Sauli kuti: “Zimene wachitazi ndi zopusa. Sunamvere lamulo limene Yehova Mulungu wako anakupatsa.+ Ukanamvera, Yehova akanachititsa kuti banja lako lilamulire Isiraeli mpaka kalekale.
3 Tsopano pita ukaphe Aamaleki+ ndiponso kuwononga+ zinthu zonse zimene ali nazo. Usakasiye aliyense.* Ukaphe+ mwamuna ndi mkazi, mwana wamngʼono ndi wakhanda, ngʼombe ndi nkhosa komanso ngamila ndi bulu.’”+