Ekisodo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zitatero, Yehova anakwiyira kwambiri Mose ndipo anati: “Kodi si paja Aroni+ Mlevi uja ndi mʼbale wako? Ndikudziwa kuti amalankhula bwino kwambiri. Ndiponso, iye ali mʼnjira kudzakuchingamira. Akakuona, adzakondwera kwambiri mumtima mwake.+ Ekisodo 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Pita kuchipululu kukachingamira Mose.”+ Choncho Aroni ananyamuka ndipo anakumana ndi Mose paphiri la Mulungu woona,+ ndipo anamulonjera nʼkumukisa.*
14 Zitatero, Yehova anakwiyira kwambiri Mose ndipo anati: “Kodi si paja Aroni+ Mlevi uja ndi mʼbale wako? Ndikudziwa kuti amalankhula bwino kwambiri. Ndiponso, iye ali mʼnjira kudzakuchingamira. Akakuona, adzakondwera kwambiri mumtima mwake.+
27 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Pita kuchipululu kukachingamira Mose.”+ Choncho Aroni ananyamuka ndipo anakumana ndi Mose paphiri la Mulungu woona,+ ndipo anamulonjera nʼkumukisa.*