1 Samueli 14:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mkazi wa Sauli dzina lake anali Ahinowamu, mwana wa Ahimazi. Mkulu wa gulu lake lankhondo anali Abineri+ mwana wa Nera, mchimwene wawo wa bambo ake a Sauli. 1 Samueli 17:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Pa nthawi imene Davide ankapita kukakumana ndi Mfilisiti uja, Sauli anafunsa Abineri,+ mkulu wa asilikali, kuti: “Abineri, kodi ameneyu ndi mwana wa ndani?”+ Abineri anayankha kuti: “Ndithu mfumu muli apa,* ine sindikudziwa.” 2 Samueli 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti,+ mwana wa Sauli, nʼkupita naye ku Mahanaimu.+ 2 Samueli 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Abineri atabwerera ku Heburoni,+ Yowabu anamʼtengera pambali kugeti kuti alankhulane naye pa awiri. Koma kumeneko anamubaya pamimba moti anafa.+ Anamupha chifukwa choti anapha Asaheli, mchimwene wake wa Yowabuyo.+
50 Mkazi wa Sauli dzina lake anali Ahinowamu, mwana wa Ahimazi. Mkulu wa gulu lake lankhondo anali Abineri+ mwana wa Nera, mchimwene wawo wa bambo ake a Sauli.
55 Pa nthawi imene Davide ankapita kukakumana ndi Mfilisiti uja, Sauli anafunsa Abineri,+ mkulu wa asilikali, kuti: “Abineri, kodi ameneyu ndi mwana wa ndani?”+ Abineri anayankha kuti: “Ndithu mfumu muli apa,* ine sindikudziwa.”
8 Koma Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti,+ mwana wa Sauli, nʼkupita naye ku Mahanaimu.+
27 Abineri atabwerera ku Heburoni,+ Yowabu anamʼtengera pambali kugeti kuti alankhulane naye pa awiri. Koma kumeneko anamubaya pamimba moti anafa.+ Anamupha chifukwa choti anapha Asaheli, mchimwene wake wa Yowabuyo.+