Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano mukadzamvera mawu anga mosamala ndi kusunga pangano langa, mudzakhaladi chuma changa chapadera pa anthu onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Deuteronomo 26:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo lero mwatsimikizira Yehova kuti mudzakhala anthu ake komanso chuma chake chapadera,+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani. Ndiponso mwamutsimikizira kuti mudzasunga malamulo ake onse.
5 Tsopano mukadzamvera mawu anga mosamala ndi kusunga pangano langa, mudzakhaladi chuma changa chapadera pa anthu onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
18 Ndipo lero mwatsimikizira Yehova kuti mudzakhala anthu ake komanso chuma chake chapadera,+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani. Ndiponso mwamutsimikizira kuti mudzasunga malamulo ake onse.