Levitiko 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Mkazi akakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, azikhala wodetsedwa kwa masiku 7. Azikhala wodetsedwa ngati mmene amakhalira pa nthawi imene akusamba.+ Levitiko 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngati mkazi akukha magazi, azikhala masiku 7 ali wodetsedwa chifukwa chakuti akusamba.+ Aliyense amene angamukhudze adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.+ Levitiko 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Usayandikire mkazi kuti ugone naye pa nthawi imene akusamba chifukwa ndi wodetsedwa.+
2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Mkazi akakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, azikhala wodetsedwa kwa masiku 7. Azikhala wodetsedwa ngati mmene amakhalira pa nthawi imene akusamba.+
19 Ngati mkazi akukha magazi, azikhala masiku 7 ali wodetsedwa chifukwa chakuti akusamba.+ Aliyense amene angamukhudze adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.+