Yoswa 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+ Yoswa 21:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kuchokera mʼfuko la Gadi,+ anawapatsa mzinda wothawirako munthu amene wapha mnzake, wa Ramoti ku Giliyadi+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Anawapatsanso Mahanaimu+ ndi malo ake odyetserako ziweto, 2 Samueli 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti,+ mwana wa Sauli, nʼkupita naye ku Mahanaimu.+
8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+
38 Kuchokera mʼfuko la Gadi,+ anawapatsa mzinda wothawirako munthu amene wapha mnzake, wa Ramoti ku Giliyadi+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Anawapatsanso Mahanaimu+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
8 Koma Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti,+ mwana wa Sauli, nʼkupita naye ku Mahanaimu.+